P IS FOR PANGOLIN: A POEM BY VIRGINIA MCKENNA

In honour of her 90th birthday, we are sharing a poem written by Virginia McKenna OBE, one of our Patrons. Following a successful career as an actress, Virginia founded the Born Free Foundation in 1984. Working to save lives, stop suffering and protect species in the wild, it is now one of the world’s most respected wildlife welfare charities. They were instrumental in the establishment of our Centre, Malawi’s first and only wildlife sanctuary.

P is for Pangolin

 

I wish I understood

Why people hurt me,

Kill me,

Eat me.

It is true, of course,

That I kill too. But ants and

Other insects.

Not creatures most people eat.

 

And I am used

For other reasons too.

For medicine –

They say my scales

Can cure heart disease

And cancer.

Of course I can’t be sure

As I’m no longer

There.

 

I wonder if, one day,

All of us will

Be gone.  Will anyone be sad?

I do try and hide

When people hurt me.

I roll into a ball.

But they still see me,

And steal me,

And kill me.

 

Not everyone is the same

I know. Some rescue me

Care for me and even

Like me.

I hope, with all my heart, that they can

Save me.

 

Do remember that

P is for Pangolin

P is for Pain

P is for Protect

PLEASE

P is for Pangolin

 

Ndikulaka-laka ndikanamvetsetsa

Chifukwa chimene anthu amandipwetekera

Amandipha

Amandidya

Ndi zoona. Inde

Kuti inenso ndimapha. Koma nyerere

Ndi zilombo zina

Osati zolengedwa zomwe anthu ambiri amadya

 

Ndipo ndimagwiritsidwa ntchito

Pa zifukwa zinanso

Cha mankhwala

Amati mamba anga

Amachiza nthenda ya mtima

Ndipo ngakhalenso nthenda ya khansa

Inde sindingatsimikize

Chifukwa sindilinso

Kumeneko

 

Ndimaganizira ngati tsiku lina

Tonsefe tidzakhala titapita. Kodi alipo amene adzakhala ndi chisoni?

Ndimayesa ndipo ndimabisala

Pamene anthu amandipweteka

Ndimazizinga ngati mpira

Koma amandionabe

Ndipo amandiba

Ndiponso amandipha

 

Sionse ndi ofanana

Ndimadziwa. Ena amandipulumutsa

Kundisamalira ndipo ngakhale

Kundikonda

Ndikukhulupirira ndi mtima wanga wonse kuti angathe

Kundipulumutsa

 

Kodi mukukumbukira kuti?

Mu chizungu chilembo P ndichoyambirira cha pangolin (ngaka)

Mu chizungu chilembo P ndichoyambirira cha pain (ululu)

Mu chizungu chilembo P ndichoyambirira cha protect (kuteteza)

PLEASE